Добавить новость
News in English
Новости сегодня

Новости от TheMoneytizer

Ulosi wa Prophet Rodrick Mtupa wakwanilitsidwa….A Polisi ayenda wa uyo! Uyo!

By Thumbiko Nyirongo

Kanema yemwe wafala kwambiri pa masamba a mchezo a Facebook ndi Whatsapp akuonetsa, munthu wa Mulungu Prophet Rodrick Mtupa, akulotsera zomwe zachitika dzulo ku Limbe mu Mzinda wa Blantyre komwe apolisi komanso ogwira ntchito ku khonsolo ya mzinda wu anayendesedwa wa uyo! Uyo! ndi anthu okwiya.

Apolisi-wa anawona za malozazi pa nthawi yomwe anapita ku msika wa Limbe ndi cholinga chokagwira a malonda (Ma Vendor) omwe amachita malonda awo m’malo osayenera; komatu phuno salota, osaka-wa anasanduka wosakidwa pomwe ochita malonda okwiya wa anayamba kuwagenda mpaka kuthawa liwilo la mtondo wodowoka.

Koma malingana ndi Kanema amene anthu akugawana pa makina a internet, zomwe zachitika ku Limbe zinalotseredwa kale ndi Prophet Mtupa a utumiki wa Holy Palace Cathedral International, kutero kuti panalibe cha chilendo.

The highly respected God’s messenger Senior Prophet Mtupa

“Kuzakhala kuukira kwa anthu; ndipo m’maso anga auzimu ndikuwona gulu la anthu litagwirana manja ndi kumagenda anthu a boma(a polisi komanso ogwira ntchito ku city), izi zichitika ndithu,” anatero Prophet Mtupa mu Ulosi wawo wa kumayambiliro a chaka chino, akulotsera zomwe zachitika dzulo lachiwiri ku Limbe.

Pakadali pano, Mneneri wa apolisi ya Limbe Aubrey Singayamwa wati apolisi akhazikitsa kafukufuku wawo kufuna kumanga anthu omwe anayambitsa ziwawazi, ndipo pofika lero lachitatu apolisi-wa sanabwere poyera kufotokoza ngati amanga munthu kapena ayi.

The post Ulosi wa Prophet Rodrick Mtupa wakwanilitsidwa….A Polisi ayenda wa uyo! Uyo! appeared first on Malawi Voice.

Читайте на сайте


Smi24.net — ежеминутные новости с ежедневным архивом. Только у нас — все главные новости дня без политической цензуры. Абсолютно все точки зрения, трезвая аналитика, цивилизованные споры и обсуждения без взаимных обвинений и оскорблений. Помните, что не у всех точка зрения совпадает с Вашей. Уважайте мнение других, даже если Вы отстаиваете свой взгляд и свою позицию. Мы не навязываем Вам своё видение, мы даём Вам срез событий дня без цензуры и без купюр. Новости, какие они есть —онлайн с поминутным архивом по всем городам и регионам России, Украины, Белоруссии и Абхазии. Smi24.net — живые новости в живом эфире! Быстрый поиск от Smi24.net — это не только возможность первым узнать, но и преимущество сообщить срочные новости мгновенно на любом языке мира и быть услышанным тут же. В любую минуту Вы можете добавить свою новость - здесь.




Новости от наших партнёров в Вашем городе

Ria.city
Музыкальные новости
Новости России
Экология в России и мире
Спорт в России и мире
Moscow.media






Топ новостей на этот час

Rss.plus





СМИ24.net — правдивые новости, непрерывно 24/7 на русском языке с ежеминутным обновлением *